Zedlyric
Dzuwa Slapdee x Jorzi Lyrics
Intro
XYZ Entertainment
Intro-Chorus(Jorzi)
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa,
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, ambuye tidaliseni ndi zduwa.
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa.
Ambuye chosani dzuwa,
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, ambuye tidaliseni ndi zduwa.
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa.
[Verse 1 -Slapdee]
Takana ku biliever ndise tili naminyama,
Navenso venzo nveka munshe vinaleka naku wama,
Tinalakwila ndani mutikambileko sorry,
Mayeso yatikonka Bad izibika story,
First yenze cholera, kwabwela loadsheding,
Before nama corona tenze busy nama gassing.
Tayambo payana teka teka its so disgusting.
Nama busa balema navo vama fasting,
Ku hood kwanga ba guy bafuna che ka certain.
Bavale che pamala naka nsima ndiye curtain.
Sibafuna navambili umoyo che ni dalisoul.
Ambuye abwezepo nga muchila wamalinso.
How did we get here nalema kuzifunsa,
Kapena niu dalo(dull) sinasilize pa UNZA
Agogo ananiuza uzakula mwana chipuba,
Vikaku vuta langa kumwamba upempe zduwa.
[Chorus – Jorzi]
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa,
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, Ambuye tidaliseni ndi zduwa.
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa.
[Verse 2- Slapdee]
Eh
Nauka mutu uzinguluka monga nenze pakampelwa,
Pa FB tayali akali kumenyana na mwelwa,
could it be that I’m stressing or making a big fuss,
I know that there’s somebody looking for a face mask,
Coz they die without a proper doctor or a nurse,
Without the medication, they will end up in a hearse,
Are we, born with a gift or maybe blessed with a curse,
With the afterlife, I’m certain we might end up in a church,
Just not longa ago nenzo nvelela seer 1,
Enze once a topic patu napa bondi panu
Since when chinfine chinankalapo big issue,
Sambani kumanja sanitize nama tissue.
Now all my shows canceled I’m living off my investments
Pray to God he save my family and my best friends,
Everything quarantined house, money, Car.
Pray for Zambia, for the globe for Africa.
Chorus(Jorzi)
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa,
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, ambuye tidaliseni ndi zduwa.
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa.
[Outro-Chorus – Jorzi]
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa,
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, ambuye tidaliseni ndi zduwa.
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa.
No comments yet